1 Samueli 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno Samueli anatenga mwana wa nkhosa woyamwa nʼkumupereka nsembe yopsereza+ yathunthu kwa Yehova. Atatero anapemphera kwa Yehova kuti athandize Aisiraeli ndipo Yehova anamuyankha.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:9 Nsanja ya Olonda,3/15/2005, tsa. 22
9 Ndiyeno Samueli anatenga mwana wa nkhosa woyamwa nʼkumupereka nsembe yopsereza+ yathunthu kwa Yehova. Atatero anapemphera kwa Yehova kuti athandize Aisiraeli ndipo Yehova anamuyankha.+