1 Samueli 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Afilisiti anagonjetsedwa ndipo sanabwerenso mʼdera la Isiraeli.+ Pa nthawi yonse imene Samueli anali moyo, Yehova sanalole kuti Afilisiti alowe mʼdera la Aisiraeli.+
13 Choncho Afilisiti anagonjetsedwa ndipo sanabwerenso mʼdera la Isiraeli.+ Pa nthawi yonse imene Samueli anali moyo, Yehova sanalole kuti Afilisiti alowe mʼdera la Aisiraeli.+