1 Samueli 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso Aisiraeli anatenga mizinda imene Afilisitiwo analanda kuyambira ku Ekironi mpaka ku Gati. Kuwonjezera pamenepo, Aisiraeli anatenganso dera lawo lomwe Afilisiti anawalanda. Komanso pakati pa Aisiraeli ndi Aamori panali mtendere.+
14 Komanso Aisiraeli anatenga mizinda imene Afilisitiwo analanda kuyambira ku Ekironi mpaka ku Gati. Kuwonjezera pamenepo, Aisiraeli anatenganso dera lawo lomwe Afilisiti anawalanda. Komanso pakati pa Aisiraeli ndi Aamori panali mtendere.+