1 Samueli 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwana wake woyamba anali Yoweli, ndipo wachiwiri anali Abiya.+ Iwo anali oweruza ku Beere-seba.