1 Samueli 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo anamuuza kuti: “Inuyo mwakalamba, koma ana anu sakutsatira chitsanzo chanu. Ndiye mutisankhire mfumu yoti izitiweruza ngati mitundu ina yonse.”+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:5 Tsanzirani, ptsa. 72-73 Nsanja ya Olonda,1/1/2011, tsa. 27
5 Iwo anamuuza kuti: “Inuyo mwakalamba, koma ana anu sakutsatira chitsanzo chanu. Ndiye mutisankhire mfumu yoti izitiweruza ngati mitundu ina yonse.”+