-
1 Samueli 8:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Koma Samueli sanasangalale atamuuza kuti: “Mutipatse mfumu yoti izitiweruza.” Kenako Samueli anapemphera kwa Yehova.
-