1 Samueli 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova anauza Samueli kuti: “Mvera zonse zimene anthuwo akuuza, chifukwatu sanakane iwe koma akana ine kuti ndikhale mfumu yawo.+
7 Yehova anauza Samueli kuti: “Mvera zonse zimene anthuwo akuuza, chifukwatu sanakane iwe koma akana ine kuti ndikhale mfumu yawo.+