1 Samueli 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zimene akuchitazi ndi zimene akhala akuchita kuyambira tsiku limene ndinawatulutsa ku Iguputo mpaka pano. Akhala akundisiya+ nʼkumatumikira milungu ina+ ndipo nʼzimenenso akuchitira iweyo.
8 Zimene akuchitazi ndi zimene akhala akuchita kuyambira tsiku limene ndinawatulutsa ku Iguputo mpaka pano. Akhala akundisiya+ nʼkumatumikira milungu ina+ ndipo nʼzimenenso akuchitira iweyo.