-
1 Samueli 8:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Adzatenganso gawo limodzi la magawo 10 alionse a zokolola zamʼminda yanu ya mpesa komanso mʼminda ya mbewu zina nʼkuzipereka kwa nduna zake ndi antchito ake.
-