1 Samueli 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pa ziweto zanu 10 zilizonse adzatengapo chiweto chimodzi+ ndipo inuyo mudzakhala antchito ake.