1 Samueli 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anali ndi mwana wamwamuna dzina lake Sauli+ ndipo anali mnyamata wooneka bwino. Mu Isiraeli munalibe mwamuna wooneka bwino kuposa iyeyu. Komanso Sauli anali wamʼtali kwambiri moti panalibe munthu aliyense amene ankapitirira mʼmapewa ake.
2 Anali ndi mwana wamwamuna dzina lake Sauli+ ndipo anali mnyamata wooneka bwino. Mu Isiraeli munalibe mwamuna wooneka bwino kuposa iyeyu. Komanso Sauli anali wamʼtali kwambiri moti panalibe munthu aliyense amene ankapitirira mʼmapewa ake.