-
1 Samueli 9:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndiyeno anayendayenda mʼdera lamapiri la Efuraimu mpaka kukafika mʼdera la Salisa, koma abuluwo sanawapeze. Atatero anafika mʼdera la Saalimu ndipo kumenekonso sanawapeze. Anafufuza dera lonse la Benjamini koma sanawapeze.
-