1 Samueli 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma iye anayankha kuti: “Mumzinda uwo muli munthu wa Mulungu ndipo anthu amamulemekeza. Zonse zimene wanena zimachitika.+ Bwanji tipite kumeneko, mwina angakatiuze kumene tingalowere.”
6 Koma iye anayankha kuti: “Mumzinda uwo muli munthu wa Mulungu ndipo anthu amamulemekeza. Zonse zimene wanena zimachitika.+ Bwanji tipite kumeneko, mwina angakatiuze kumene tingalowere.”