-
1 Samueli 9:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Koma Sauli anafunsa wantchito wakeyo kuti: “Tikapita kumeneko tikamʼpatsa chiyani? Tilibe chakudya chilichonse kapena mphatso yoti tikamʼpatse munthu wa Mulungu woonayo. Nanga tili ndi chilichonse ngati?”
-