1 Samueli 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 (Kalekale mu Isiraeli, munthu akafuna kukafunsira kwa Mulungu ankanena kuti: “Tiyeni tipite kwa wamasomphenya.”+ Chifukwa kalelo mneneri ankatchedwa wamasomphenya.) 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:9 Nsanja ya Olonda,3/15/2005, tsa. 22
9 (Kalekale mu Isiraeli, munthu akafuna kukafunsira kwa Mulungu ankanena kuti: “Tiyeni tipite kwa wamasomphenya.”+ Chifukwa kalelo mneneri ankatchedwa wamasomphenya.)