1 Samueli 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo anawayankha kuti: “Inde, alipo. Ali kumene mukuloweraku. Fulumirani, wafika lero lomwe mumzindawu chifukwa lero anthu akupereka nsembe+ pamalo okwezeka.+
12 Iwo anawayankha kuti: “Inde, alipo. Ali kumene mukuloweraku. Fulumirani, wafika lero lomwe mumzindawu chifukwa lero anthu akupereka nsembe+ pamalo okwezeka.+