-
1 Samueli 9:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Mukangolowa mumzinda, mumʼpeza asanapite kukadya kumalo okwezeka. Anthu sangayambe kudya pokhapokha iye atafika, chifukwa iyeyo ndi amene amadalitsa nsembeyo. Akatero oitanidwa amadya. Ndiye pitani musachedwe, mumʼpeza.”
-