1 Samueli 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Samueli ataona Sauli, Yehova anamuuza kuti: “Munthu amene ndinakuuza uja ndi ameneyu. Uja ndinati, ‘Ndi amene adzalamulire anthu anga.’”+
17 Samueli ataona Sauli, Yehova anamuuza kuti: “Munthu amene ndinakuuza uja ndi ameneyu. Uja ndinati, ‘Ndi amene adzalamulire anthu anga.’”+