1 Samueli 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Samueli anayankha Sauli kuti: “Wamasomphenyayo ndineyo. Tiyeni tsogolani tipite kumalo okwezeka ndipo mudya ndi ine lero.+ Ndidzakulolani kupita kwanu mawa mʼmawa ndipo ndikuuzani zonse zimene mukufuna kudziwa.*
19 Samueli anayankha Sauli kuti: “Wamasomphenyayo ndineyo. Tiyeni tsogolani tipite kumalo okwezeka ndipo mudya ndi ine lero.+ Ndidzakulolani kupita kwanu mawa mʼmawa ndipo ndikuuzani zonse zimene mukufuna kudziwa.*