-
1 Samueli 9:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Wophikayo anatenga mwendo wonse nʼkumupatsa Sauli. Kenako Samueli anati: “Nyama imene inasungidwa ndi imeneyi. Idya. Anasungira iweyo kuti udye pa nthawi ya mwambowu chifukwa ndinawauza kuti, ‘Ndaitana alendo.’” Choncho Sauli anadyera limodzi ndi Samueli pa tsikulo.
-