-
1 Samueli 9:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Samueli ndi Sauli anadzuka mʼmawa kwambiri ndipo mʼbandakucha, Samueli ali padenga la nyumba, anaitana Sauli nʼkumuuza kuti: “Konzeka ndikuperekeze.” Choncho Sauli anakonzeka ndipo iyeyo ndi Samueli anatuluka panja.
-