-
1 Samueli 10:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Sauli atangosiyana ndi Samueli, Mulungu anayamba kusintha mtima wake kukhala ngati wa munthu wina, moti zinthu zonse zija zinachitikadi tsiku limenelo.
-