1 Samueli 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako anabweretsa pafupi fuko la Benjamini potengera mabanja awo ndipo banja la Amatiri linasankhidwa. Pomaliza, Sauli mwana wa Kisi anasankhidwa.+ Koma atamufufuza, sanamupeze.
21 Kenako anabweretsa pafupi fuko la Benjamini potengera mabanja awo ndipo banja la Amatiri linasankhidwa. Pomaliza, Sauli mwana wa Kisi anasankhidwa.+ Koma atamufufuza, sanamupeze.