1 Samueli 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho anafunsanso Yehova kuti:+ “Kodi munthu ameneyu wafika kale pano?” Yehova anayankha kuti: “Uyo wabisala pakati pa katunduyo.”
22 Choncho anafunsanso Yehova kuti:+ “Kodi munthu ameneyu wafika kale pano?” Yehova anayankha kuti: “Uyo wabisala pakati pa katunduyo.”