1 Samueli 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho anthu anathamanga nʼkukamutenga. Ataimirira pakati pa anthuwo, ankaoneka wamtali kwambiri moti palibe aliyense amene ankapitirira mʼmapewa ake.+
23 Choncho anthu anathamanga nʼkukamutenga. Ataimirira pakati pa anthuwo, ankaoneka wamtali kwambiri moti palibe aliyense amene ankapitirira mʼmapewa ake.+