1 Samueli 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Samueli anauza anthu onsewo kuti: “Kodi mwaona munthu amene Yehova wamusankha,+ kuti palibe aliyense wofanana naye?” Anthu onsewo anayamba kufuula kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”
24 Ndiyeno Samueli anauza anthu onsewo kuti: “Kodi mwaona munthu amene Yehova wamusankha,+ kuti palibe aliyense wofanana naye?” Anthu onsewo anayamba kufuula kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”