1 Samueli 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Samueli anauza anthuwo zinthu zimene mfumu iyenera kulandira kwa iwo+ ndipo anazilemba mʼbuku nʼkuliika mʼchihema cha Yehova. Kenako Samueli anauza anthuwo kuti abwerere kwawo.
25 Samueli anauza anthuwo zinthu zimene mfumu iyenera kulandira kwa iwo+ ndipo anazilemba mʼbuku nʼkuliika mʼchihema cha Yehova. Kenako Samueli anauza anthuwo kuti abwerere kwawo.