1 Samueli 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma anthu ena opanda pake ankanena kuti: “Kodi ameneyu angathedi kutipulumutsa?”+ Choncho anayamba kumunyoza, moti sanamʼbweretsere mphatso iliyonse.+ Koma Sauli sanayankhe chilichonse.*
27 Koma anthu ena opanda pake ankanena kuti: “Kodi ameneyu angathedi kutipulumutsa?”+ Choncho anayamba kumunyoza, moti sanamʼbweretsere mphatso iliyonse.+ Koma Sauli sanayankhe chilichonse.*