-
1 Samueli 11:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndiyeno Sauli anatulukira kuchokera kubusa akukusa ziweto ndipo anafunsa kuti: “Kodi chachitika nʼchiyani? Anthuwa akulira chiyani?” Choncho anamufotokozera zimene anthu a ku Yabesi ananena.
-