1 Samueli 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sauli atamva zimenezo, mzimu wa Mulungu unamʼpatsa mphamvu+ ndipo anapsa mtima kwambiri.