1 Samueli 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho anthu onse anapita ku Giligala ndipo analonga Sauli ufumu pamaso pa Yehova. Kenako anapereka kwa Yehova nsembe zamgwirizano+ ndipo Sauli ndi amuna onse a Isiraeli anasangalala kwambiri.+
15 Choncho anthu onse anapita ku Giligala ndipo analonga Sauli ufumu pamaso pa Yehova. Kenako anapereka kwa Yehova nsembe zamgwirizano+ ndipo Sauli ndi amuna onse a Isiraeli anasangalala kwambiri.+