1 Samueli 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano mfumu ija ndi imeneyi, yomwe ikukutsogoleraniyi.*+ Koma ine ndakalamba ndipo tsitsi langa lachita imvi. Ana anga aamuna ndi awa muli nawowa+ ndipo ine ndakutsogolerani kuyambira ndili kamnyamata mpaka lero.+
2 Tsopano mfumu ija ndi imeneyi, yomwe ikukutsogoleraniyi.*+ Koma ine ndakalamba ndipo tsitsi langa lachita imvi. Ana anga aamuna ndi awa muli nawowa+ ndipo ine ndakutsogolerani kuyambira ndili kamnyamata mpaka lero.+