1 Samueli 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Samueli anauza anthuwo kuti: “Yehova, amene anagwiritsa ntchito Mose ndi Aroni, amenenso anatulutsa makolo anu mʼdziko la Iguputo,+ ndi mboni.
6 Choncho Samueli anauza anthuwo kuti: “Yehova, amene anagwiritsa ntchito Mose ndi Aroni, amenenso anatulutsa makolo anu mʼdziko la Iguputo,+ ndi mboni.