-
1 Samueli 12:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Tsopano bwerani pafupi kuti ndikuweruzeni pamaso pa Yehova mogwirizana ndi ntchito zonse zolungama zimene Yehova wachitira inuyo komanso makolo anu.
-