1 Samueli 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yakobo atangofika ku Iguputo,+ makolo anu nʼkuyamba kupempha Yehova kuti awathandize,+ Yehova anatumiza Mose+ ndi Aroni kuti atsogolere makolo anu pochoka ku Iguputo kuti azikhala mʼdzikoli.+
8 Yakobo atangofika ku Iguputo,+ makolo anu nʼkuyamba kupempha Yehova kuti awathandize,+ Yehova anatumiza Mose+ ndi Aroni kuti atsogolere makolo anu pochoka ku Iguputo kuti azikhala mʼdzikoli.+