1 Samueli 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma iwo anaiwala Yehova Mulungu wawo ndipo iye anawapereka*+ kwa Sisera+ mkulu wa asilikali a Hazori, komanso kwa Afilisiti+ ndi kwa mfumu ya Mowabu,+ ndipo onsewa anamenyana nawo.
9 Koma iwo anaiwala Yehova Mulungu wawo ndipo iye anawapereka*+ kwa Sisera+ mkulu wa asilikali a Hazori, komanso kwa Afilisiti+ ndi kwa mfumu ya Mowabu,+ ndipo onsewa anamenyana nawo.