1 Samueli 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Yehova anatumiza Yerubaala,+ Bedani, Yefita+ ndi Samueli+ ndipo anakupulumutsani kwa adani anu onse okuzungulirani kuti mukhale pa mtendere.+
11 Kenako Yehova anatumiza Yerubaala,+ Bedani, Yefita+ ndi Samueli+ ndipo anakupulumutsani kwa adani anu onse okuzungulirani kuti mukhale pa mtendere.+