1 Samueli 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mutaona kuti Nahasi,+ mfumu ya Aamoni, wabwera kudzamenyana nanu, munayamba kundiuza kuti, ‘Ayi, ife tikufuna mfumu basi,’+ ngakhale kuti Mfumu yanu ndi Yehova Mulungu wanu.+
12 Mutaona kuti Nahasi,+ mfumu ya Aamoni, wabwera kudzamenyana nanu, munayamba kundiuza kuti, ‘Ayi, ife tikufuna mfumu basi,’+ ngakhale kuti Mfumu yanu ndi Yehova Mulungu wanu.+