1 Samueli 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngati mudzaopa Yehova,+ kumutumikira+ ndiponso kumumvera,+ ngati simudzasiya malamulo a Yehova komanso ngati inuyo ndi mfumu yanu mudzatsatira Yehova Mulungu wanu, zili bwino.
14 Ngati mudzaopa Yehova,+ kumutumikira+ ndiponso kumumvera,+ ngati simudzasiya malamulo a Yehova komanso ngati inuyo ndi mfumu yanu mudzatsatira Yehova Mulungu wanu, zili bwino.