1 Samueli 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma mukasiya kumvera Yehova ndiponso kutsatira malamulo a Yehova, dzanja la Yehova lidzakulangani inuyo komanso abambo anu.+
15 Koma mukasiya kumvera Yehova ndiponso kutsatira malamulo a Yehova, dzanja la Yehova lidzakulangani inuyo komanso abambo anu.+