-
1 Samueli 12:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Choncho Samueli anapemphera kwa Yehova ndipo Yehova anabweretsa mabingu ndi mvula tsiku limenelo. Anthu onse anachita mantha kwambiri ndi Yehova ndiponso Samueli.
-