1 Samueli 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zitatero, anthu onse anauza Samueli kuti: “Tipempherereni ife atumiki anu kwa Yehova Mulungu wanu,+ chifukwa sitikufuna kufa. Tawonjezera choipa china pa machimo athu popempha kuti tikhale ndi mfumu.”
19 Zitatero, anthu onse anauza Samueli kuti: “Tipempherereni ife atumiki anu kwa Yehova Mulungu wanu,+ chifukwa sitikufuna kufa. Tawonjezera choipa china pa machimo athu popempha kuti tikhale ndi mfumu.”