1 Samueli 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Samueli anawauza kuti: “Musachite mantha. Nʼzoona kuti mwachita zoipa zonsezi. Koma ngakhale zili choncho, musasiye kutsatira Yehova.+ Muzitumikira Yehova ndi mtima wanu wonse.+
20 Koma Samueli anawauza kuti: “Musachite mantha. Nʼzoona kuti mwachita zoipa zonsezi. Koma ngakhale zili choncho, musasiye kutsatira Yehova.+ Muzitumikira Yehova ndi mtima wanu wonse.+