1 Samueli 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Musapatuke nʼkuyamba kutsatira milungu yopanda pake*+ yomwe ndi yosathandiza+ komanso singakupulumutseni chifukwa ndi yopanda pake.* 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:21 Nsanja ya Olonda,7/15/2011, ptsa. 13-14
21 Musapatuke nʼkuyamba kutsatira milungu yopanda pake*+ yomwe ndi yosathandiza+ komanso singakupulumutseni chifukwa ndi yopanda pake.*