-
1 Samueli 12:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Komanso nʼzosatheka kuti ineyo ndichimwire Yehova posiya kukupemphererani. Ndipo ndipitiriza kukulangizani za njira yabwino ndi yolondola.
-