1 Samueli 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo amuna a Isiraeli anaona kuti zinthu zavuta chifukwa anapanikizika kwambiri. Anthu anakabisala mʼmapanga,+ mʼmaenje, mʼmatanthwe, mʼzipinda zapansi ndi mʼzitsime zopanda madzi.
6 Ndipo amuna a Isiraeli anaona kuti zinthu zavuta chifukwa anapanikizika kwambiri. Anthu anakabisala mʼmapanga,+ mʼmaenje, mʼmatanthwe, mʼzipinda zapansi ndi mʼzitsime zopanda madzi.