1 Samueli 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aheberi ena mpaka anawoloka Yorodano nʼkupita mʼdera la Gadi ndi Giliyadi.+ Koma Sauli anali adakali ku Giligala ndipo anthu onse amene ankamutsatira ankanjenjemera.
7 Aheberi ena mpaka anawoloka Yorodano nʼkupita mʼdera la Gadi ndi Giliyadi.+ Koma Sauli anali adakali ku Giligala ndipo anthu onse amene ankamutsatira ankanjenjemera.