-
1 Samueli 13:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Sauli anapitiriza kudikira kwa masiku 7 mpaka nthawi imene anagwirizana ndi Samueli. Koma Samueli sanafikebe ku Giligala ndipo anthu anayamba kubalalika kumusiya Sauli.
-