1 Samueli 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Samueli anati: “Ndiye chiyani wachitachi?” Sauli anayankha kuti: “Ndinaona kuti anthu akubalalika kundisiya ndekha,+ ndipo inu simunabwere pa nthawi imene tinagwirizana ija. Ndinaonanso kuti Afilisiti akusonkhana ku Mikimasi.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:11 Nsanja ya Olonda,8/1/2000, ptsa. 12-13
11 Ndiyeno Samueli anati: “Ndiye chiyani wachitachi?” Sauli anayankha kuti: “Ndinaona kuti anthu akubalalika kundisiya ndekha,+ ndipo inu simunabwere pa nthawi imene tinagwirizana ija. Ndinaonanso kuti Afilisiti akusonkhana ku Mikimasi.+