1 Samueli 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma tsopano ufumu wako sukhalitsa.+ Yehova apeza munthu wapamtima pake,+ ndipo Yehova amuika kukhala mtsogoleri wa anthu ake+ chifukwa iwe sunamvere zimene Yehova anakulamula.”+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:14 Nsanja ya Olonda,9/1/2011, ptsa. 26-291/1/1989, tsa. 23
14 Koma tsopano ufumu wako sukhalitsa.+ Yehova apeza munthu wapamtima pake,+ ndipo Yehova amuika kukhala mtsogoleri wa anthu ake+ chifukwa iwe sunamvere zimene Yehova anakulamula.”+